Wopani Mulungu ndi kumutamanda Mngeloyo anayankhula mokweza mawu kuti, “chifukwa nthawi yoweruza anthu yafika. Mumupembedze Iye amene analenga thambo, dziko lapansi, nyanja ndi akasupe amadzi.” Post Views: 0